Yeremiya 32:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 ‘Mzinda uwu wakhala chinthu chimene chimandikwiyitsa komanso kundipsetsa mtima kungoyambira pamene unamangidwa mpaka lero.+ Choncho ukuyenera kuchotsedwa pamaso panga+
31 ‘Mzinda uwu wakhala chinthu chimene chimandikwiyitsa komanso kundipsetsa mtima kungoyambira pamene unamangidwa mpaka lero.+ Choncho ukuyenera kuchotsedwa pamaso panga+