Yeremiya 32:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 chifukwa cha zoipa zonse zimene Aisiraeli ndi Ayuda achita nʼkundikhumudwitsa nazo. Achita zimenezi pamodzi ndi mafumu awo,+ akalonga awo,+ ansembe awo, aneneri awo,+ anthu a ku Yuda ndi anthu onse amene akukhala mu Yerusalemu.
32 chifukwa cha zoipa zonse zimene Aisiraeli ndi Ayuda achita nʼkundikhumudwitsa nazo. Achita zimenezi pamodzi ndi mafumu awo,+ akalonga awo,+ ansembe awo, aneneri awo,+ anthu a ku Yuda ndi anthu onse amene akukhala mu Yerusalemu.