Yeremiya 32:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 ‘Ine ndidzawasonkhanitsa pamodzi kuchokera kumayiko onse kumene ndinawabalalitsira nditakwiya, kupsa mtima ndiponso ndili ndi ukali waukulu.+ Ndidzawabwezeretsa mʼdziko lino nʼkuwachititsa kuti azikhala motetezeka.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:37 Nsanja ya Olonda,3/15/1995, ptsa. 13-14
37 ‘Ine ndidzawasonkhanitsa pamodzi kuchokera kumayiko onse kumene ndinawabalalitsira nditakwiya, kupsa mtima ndiponso ndili ndi ukali waukulu.+ Ndidzawabwezeretsa mʼdziko lino nʼkuwachititsa kuti azikhala motetezeka.+