Yeremiya 32:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Ndidzawapatsa mtima umodzi+ komanso kuwachititsa kuti aziyenda mʼnjira imodzi kuti azindiopa nthawi zonse. Ndidzachita zimenezi kuti iwo limodzi ndi ana awo zinthu ziziwayendera bwino.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:39 Nsanja ya Olonda,3/15/1995, ptsa. 13-15
39 Ndidzawapatsa mtima umodzi+ komanso kuwachititsa kuti aziyenda mʼnjira imodzi kuti azindiopa nthawi zonse. Ndidzachita zimenezi kuti iwo limodzi ndi ana awo zinthu ziziwayendera bwino.+