Yeremiya 32:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Ndidzachita nawo pangano+ lomwe lidzakhalapo mpaka kalekale. Panganoli lidzakhala lakuti sindidzasiya kuwachitira zinthu zabwino+ ndipo ndidzawapatsa mtima woti azindiopa kuti asachoke kwa ine.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:40 Nsanja ya Olonda,3/15/1995, ptsa. 13-15
40 Ndidzachita nawo pangano+ lomwe lidzakhalapo mpaka kalekale. Panganoli lidzakhala lakuti sindidzasiya kuwachitira zinthu zabwino+ ndipo ndidzawapatsa mtima woti azindiopa kuti asachoke kwa ine.+