Yeremiya 32:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndidzasangalala nawo ndipo ndidzawachitira zabwino.+ Ndidzawachititsa kuti azikhala mʼdziko lino+ mpaka kalekale. Ndidzachita zimenezi ndi mtima wanga wonse komanso moyo wanga wonse.’”
41 Ndidzasangalala nawo ndipo ndidzawachitira zabwino.+ Ndidzawachititsa kuti azikhala mʼdziko lino+ mpaka kalekale. Ndidzachita zimenezi ndi mtima wanga wonse komanso moyo wanga wonse.’”