Yeremiya 32:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Anthu adzagulanso minda mʼdziko lino,+ ngakhale mukunena kuti: “Dziko ili ndi bwinja, lopanda munthu wokhalamo kapena nyama yakutchire ndipo laperekedwa kwa Akasidi.”’
43 Anthu adzagulanso minda mʼdziko lino,+ ngakhale mukunena kuti: “Dziko ili ndi bwinja, lopanda munthu wokhalamo kapena nyama yakutchire ndipo laperekedwa kwa Akasidi.”’