Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 32:44
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 44 ‘Anthu adzagula minda ndi ndalama ndipo adzalemberana makalata a pangano pamaso pa mboni ndi kumata makalatawo. Zimenezi zidzachitika mʼdziko la Benjamini,+ mʼmadera ozungulira Yerusalemu, mʼmizinda ya Yuda,+ mʼmizinda yamʼmadera amapiri, mʼmizinda yamʼchigwa ndi mʼmizinda yakumʼmwera.+ Zidzakhala choncho chifukwa ndidzabwezeretsa anthu ake amene anatengedwa kupita kudziko lina,’+ akutero Yehova.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena