Yeremiya 33:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 ‘Mundiitane ndipo ndidzakuyankhani. Nthawi yomweyo ndidzakuuzani zinthu zazikulu ndi zovuta kuzimvetsa zimene simukuzidziwa.’”+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 33:3 Yeremiya, ptsa. 114-115
3 ‘Mundiitane ndipo ndidzakuyankhani. Nthawi yomweyo ndidzakuuzani zinthu zazikulu ndi zovuta kuzimvetsa zimene simukuzidziwa.’”+