Yeremiya 33:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena mawu okhudza nyumba zamumzinda uwu ndiponso okhudza nyumba za mafumu a Yuda, zimene zagwetsedwa chifukwa cha malo okwera omenyerapo nkhondo ndiponso lupanga la adani.+
4 “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena mawu okhudza nyumba zamumzinda uwu ndiponso okhudza nyumba za mafumu a Yuda, zimene zagwetsedwa chifukwa cha malo okwera omenyerapo nkhondo ndiponso lupanga la adani.+