-
Yeremiya 33:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Wanenanso mawu okhudza anthu amene akubwera kudzamenyana ndi Akasidi komanso zokhudza malo amene adzaza ndi mitembo ya anthu amene ndawapha chifukwa cha mkwiyo wanga waukulu, omwe kuipa kwawo kwachititsa kuti mzindawu ndiubisire nkhope yanga. Iye wanena kuti:
-