-
Yeremiya 33:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 phokoso la chikondwerero ndi chisangalalo.+ Mudzamvekanso mawu a mkwati ndi mawu a mkwatibwi komanso mawu a anthu amene akunena kuti: “Yamikani Yehova wa magulu ankhondo akumwamba chifukwa Yehova ndi wabwino+ ndipo chikondi chake chokhulupirika chidzakhalapo mpaka kalekale!”’+
‘Anthuwo adzabweretsa nsembe zoyamikira kunyumba ya Yehova,+ chifukwa ndidzabwezeretsa anthu amʼdzikoli, amene anatengedwa kupita kudziko lina, kuti akhalenso ngati mmene analili poyamba,’ akutero Yehova.”
-