-
Yeremiya 34:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Koma iwe Zedekiya mfumu ya Yuda, imva mawu a Yehova akuti, ‘Ponena za iwe, Yehova wanena kuti: “Sudzafa ndi lupanga.
-