-
Yeremiya 34:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Koma patapita nthawi, iwo anakatenganso akapolo aamuna ndi aakazi amene anawamasula aja ndipo anawakakamiza kuti akhalenso akapolo awo.
-