Yeremiya 34:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndidzawapereka mʼmanja mwa adani awo ndi mʼmanja mwa onse amene akufuna moyo wawo. Mitembo yawo idzakhala chakudya cha mbalame zouluka mumlengalenga ndi zilombo zakutchire.+
20 Ndidzawapereka mʼmanja mwa adani awo ndi mʼmanja mwa onse amene akufuna moyo wawo. Mitembo yawo idzakhala chakudya cha mbalame zouluka mumlengalenga ndi zilombo zakutchire.+