Yeremiya 34:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipo Mfumu Zedekiya ya Yuda ndi akalonga ake ndidzawapereka mʼmanja mwa adani awo, mʼmanja mwa anthu amene akufuna moyo wawo ndiponso mʼmanja mwa asilikali a mfumu ya ku Babulo+ amene akubwerera osamenyana nanu.’+
21 Ndipo Mfumu Zedekiya ya Yuda ndi akalonga ake ndidzawapereka mʼmanja mwa adani awo, mʼmanja mwa anthu amene akufuna moyo wawo ndiponso mʼmanja mwa asilikali a mfumu ya ku Babulo+ amene akubwerera osamenyana nanu.’+