-
Yeremiya 35:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 nʼkuwabweretsa mʼnyumba ya Yehova. Ndinalowa nawo mʼchipinda chodyera cha ana a Hanani mwana wa Igadaliya, munthu wa Mulungu woona. Chipinda chimenechi chinali pafupi ndi chipinda chodyera cha akalonga chimene chinali pamwamba pa chipinda chodyera cha Maaseya mwana wa Salumu, amene anali mlonda wapakhomo.
-