Yeremiya 35:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma pamene Mfumu Nebukadinezara* ya Babulo inabwera kudzaukira dzikoli+ tinati, ‘Tiyeni tipite ku Yerusalemu kuti tithawe asilikali a Akasidi ndi asilikali a ku Siriya,’ ndipo pano tikukhala ku Yerusalemu.”
11 Koma pamene Mfumu Nebukadinezara* ya Babulo inabwera kudzaukira dzikoli+ tinati, ‘Tiyeni tipite ku Yerusalemu kuti tithawe asilikali a Akasidi ndi asilikali a ku Siriya,’ ndipo pano tikukhala ku Yerusalemu.”