Yeremiya 35:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Sipadzalephera kukhala munthu wa mʼbanja la Yehonadabu* mwana wa Rekabu woti azitumikira pamaso panga nthawi zonse.”’” Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 35:19 Yeremiya, ptsa. 159-160
19 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Sipadzalephera kukhala munthu wa mʼbanja la Yehonadabu* mwana wa Rekabu woti azitumikira pamaso panga nthawi zonse.”’”