29 Ponena za Yehoyakimu mfumu ya Yuda unene kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Iwe wawotcha mpukutuwu nʼkunena kuti, ‘Nʼchifukwa chiyani walemba mumpukutuwu kuti: “Mfumu ya Babulo idzabwera ndithu kudzawononga dziko lino ndipo simudzapezeka nyama ndi munthu wokhalamo”?’+