Yeremiya 37:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Ndiyeno Mfumu Zedekiya+ mwana wa Yosiya inayamba kulamulira mʼmalo mwa Koniya+ mwana wa Yehoyakimu chifukwa Mfumu Nebukadinezara* ya Babulo inamuika kuti akhale mfumu mʼdziko la Yuda.+
37 Ndiyeno Mfumu Zedekiya+ mwana wa Yosiya inayamba kulamulira mʼmalo mwa Koniya+ mwana wa Yehoyakimu chifukwa Mfumu Nebukadinezara* ya Babulo inamuika kuti akhale mfumu mʼdziko la Yuda.+