Yeremiya 37:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno Mfumu Zedekiya inatuma Yehukali+ mwana wa Selemiya ndi Zefaniya+ mwana wa Maaseya wansembe kwa mneneri Yeremiya kukamuuza kuti: “Chonde, tipempherere kwa Yehova Mulungu wathu.”
3 Ndiyeno Mfumu Zedekiya inatuma Yehukali+ mwana wa Selemiya ndi Zefaniya+ mwana wa Maaseya wansembe kwa mneneri Yeremiya kukamuuza kuti: “Chonde, tipempherere kwa Yehova Mulungu wathu.”