Yeremiya 37:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno asilikali a Farao anabwera kuchokera ku Iguputo+ ndipo Akasidi amene anali atazungulira mzinda wa Yerusalemu atamva zimenezi anachoka ku Yerusalemu.+
5 Ndiyeno asilikali a Farao anabwera kuchokera ku Iguputo+ ndipo Akasidi amene anali atazungulira mzinda wa Yerusalemu atamva zimenezi anachoka ku Yerusalemu.+