Yeremiya 37:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ngakhale mutapha pafupifupi asilikali onse a Akasidi amene akumenyana nanu nʼkungotsala ovulala kwambiri okha, iwo angadzukebe mʼmatenti awo nʼkuwotcha mzindawu ndi moto.”’”+
10 Ngakhale mutapha pafupifupi asilikali onse a Akasidi amene akumenyana nanu nʼkungotsala ovulala kwambiri okha, iwo angadzukebe mʼmatenti awo nʼkuwotcha mzindawu ndi moto.”’”+