Yeremiya 37:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiye ndimvereni chonde, mbuyanga mfumu. Chonde, imvani pempho langa lakuti mundikomere mtima. Musandibwezere kunyumba ya Yehonatani+ mlembi, chifukwa ndingakafere kumeneko.”+
20 Ndiye ndimvereni chonde, mbuyanga mfumu. Chonde, imvani pempho langa lakuti mundikomere mtima. Musandibwezere kunyumba ya Yehonatani+ mlembi, chifukwa ndingakafere kumeneko.”+