Yeremiya 38:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Yehova wanena kuti, ‘Amene atsale mumzinda uno adzafa ndi lupanga, njala ndi mliri.*+ Koma amene adzadzipereke* kwa Akasidi adzapitiriza kukhala ndi moyo. Adzapulumutsa moyo wake, sadzafa ayi.’+
2 “Yehova wanena kuti, ‘Amene atsale mumzinda uno adzafa ndi lupanga, njala ndi mliri.*+ Koma amene adzadzipereke* kwa Akasidi adzapitiriza kukhala ndi moyo. Adzapulumutsa moyo wake, sadzafa ayi.’+