Yeremiya 38:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova wanena kuti, ‘Mzinda uno udzaperekedwa ndithu mʼmanja mwa asilikali a mfumu ya Babulo ndipo mfumuyo idzaulanda.’”+
3 Yehova wanena kuti, ‘Mzinda uno udzaperekedwa ndithu mʼmanja mwa asilikali a mfumu ya Babulo ndipo mfumuyo idzaulanda.’”+