Yeremiya 38:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Akalonga anauza mfumu kuti: “Chonde lamulani kuti munthu uyu aphedwe+ chifukwa akufooketsa asilikali amene atsala mumzinda uno komanso anthu onse, powauza mawu amenewa. Munthu ameneyu sakuwafunira mtendere anthuwa, koma akuwafunira tsoka.”
4 Akalonga anauza mfumu kuti: “Chonde lamulani kuti munthu uyu aphedwe+ chifukwa akufooketsa asilikali amene atsala mumzinda uno komanso anthu onse, powauza mawu amenewa. Munthu ameneyu sakuwafunira mtendere anthuwa, koma akuwafunira tsoka.”