-
Yeremiya 38:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Kenako mfumu inalamula Ebedi-meleki wa ku Itiyopiya kuti: “Tenga amuna 30 kunoko, ndipo mukatulutse mneneri Yeremiya mʼchitsimemo asanafe.”
-