-
Yeremiya 38:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Ndiyeno Ebedi-meleki wa ku Itiyopiya anauza Yeremiya kuti: “Nsanza komanso nsalu zakuthazo uzikulunge kuzingwezo nʼkuziika mʼkhwapa.” Yeremiya anachitadi zimenezo,
-