Yeremiya 38:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 ndipo iwo anakoka Yeremiya ndi zingwezo nʼkumutulutsa mʼchitsimemo. Yeremiya anapitiriza kukhala mʼBwalo la Alonda.+
13 ndipo iwo anakoka Yeremiya ndi zingwezo nʼkumutulutsa mʼchitsimemo. Yeremiya anapitiriza kukhala mʼBwalo la Alonda.+