-
Yeremiya 38:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Mfumu Zedekiya inatumiza anthu kuti akaitane mneneri Yeremiya kuti abwere kwa iye pakhomo lachitatu lamʼnyumba ya Yehova. Yeremiya atafika, mfumu inamuuza kuti: “Ndikufuna ndikufunse zinazake. Usandibisire kalikonse.”
-