-
Yeremiya 38:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Koma Yeremiya anauza mfumuyo kuti: “Sadzakuperekani mʼmanja mwawo. Chonde, mverani mawu a Yehova amene ndikukuuzani. Mukatero zinthu zidzakuyenderani bwino ndipo mudzakhalabe ndi moyo.
-