Yeremiya 38:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Akazi anu onse ndi ana anu aamuna akupita nawo kwa Akasidi ndipo inuyo simudzathawa mʼmanja mwawo. Koma mfumu ya Babulo+ idzakugwirani ndipo mzindawu udzawotchedwa chifukwa cha inu.”+
23 Akazi anu onse ndi ana anu aamuna akupita nawo kwa Akasidi ndipo inuyo simudzathawa mʼmanja mwawo. Koma mfumu ya Babulo+ idzakugwirani ndipo mzindawu udzawotchedwa chifukwa cha inu.”+