Yeremiya 38:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ngati akalonga atamva kuti ndalankhula nawe, nʼkubwera kwa iwe kudzakuuza kuti, ‘Chonde tiuze zimene unalankhula ndi mfumu, usatibisire kalikonse ndipo sitikupha.+ Kodi mfumu yakuuza chiyani?’
25 Ngati akalonga atamva kuti ndalankhula nawe, nʼkubwera kwa iwe kudzakuuza kuti, ‘Chonde tiuze zimene unalankhula ndi mfumu, usatibisire kalikonse ndipo sitikupha.+ Kodi mfumu yakuuza chiyani?’