Yeremiya 38:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Uwauze kuti, ‘Ndimapempha mfumu kuti isandibwezere kunyumba ya Yehonatani chifukwa ndingakafere kumeneko.’”+
26 Uwauze kuti, ‘Ndimapempha mfumu kuti isandibwezere kunyumba ya Yehonatani chifukwa ndingakafere kumeneko.’”+