-
Yeremiya 38:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Patapita nthawi, akalonga onse anafika kwa Yeremiya nʼkumufunsa mafunso. Yeremiya anawayankha mogwirizana ndi zonse zimene mfumu inamulamula kuti anene. Choncho akalongawo sananenenso chilichonse chifukwa sanamve zimene anakambirana.
-