Yeremiya 39:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 ‘Chifukwa ine ndidzakupulumutsa ndithu ndipo sudzaphedwa ndi lupanga. Udzapulumuka+ chifukwa chakuti wandikhulupirira,’+ akutero Yehova.” Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 39:18 Nsanja ya Olonda,5/1/2012, tsa. 31
18 ‘Chifukwa ine ndidzakupulumutsa ndithu ndipo sudzaphedwa ndi lupanga. Udzapulumuka+ chifukwa chakuti wandikhulupirira,’+ akutero Yehova.”