-
Yeremiya 40:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
40 Awa ndi mawu amene Yehova anauza Yeremiya pambuyo poti Nebuzaradani+ mkulu wa asilikali olondera mfumu wamumasula kuchoka ku Rama.+ Nebuzaradani anatenga Yeremiya kumeneko atamangidwa maunyolo amʼmanja ndipo anali mʼgulu la anthu onse a ku Yerusalemu ndi a ku Yuda amene anatengedwa kupita ku ukapolo ku Babulo.
-