Yeremiya 40:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 ndipo Yehova wabweretsadi tsokali mogwirizana ndi zimene ananenazo, chifukwa anthu inu munachimwira Yehova ndipo simunamvere mawu ake. Nʼchifukwa chake zimenezi zakuchitikirani.+
3 ndipo Yehova wabweretsadi tsokali mogwirizana ndi zimene ananenazo, chifukwa anthu inu munachimwira Yehova ndipo simunamvere mawu ake. Nʼchifukwa chake zimenezi zakuchitikirani.+