Yeremiya 40:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho Yeremiya anapita ku Mizipa+ kwa Gedaliya, mwana wa Ahikamu nʼkumakhala naye limodzi ndi anthu amene anatsala mʼdziko la Yuda.
6 Choncho Yeremiya anapita ku Mizipa+ kwa Gedaliya, mwana wa Ahikamu nʼkumakhala naye limodzi ndi anthu amene anatsala mʼdziko la Yuda.