-
Yeremiya 40:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Patapita nthawi, akuluakulu onse a asilikali amene anali mʼdziko lonselo limodzi ndi asilikali awo, anamva kuti mfumu ya Babulo yaika Gedaliya mwana wa Ahikamu kuti akhale wolamulira dzikolo. Anamvanso kuti yamuika kuti azilamulira amuna, akazi ndi ana ochokera pakati pa anthu osauka mʼdzikolo amene sanatengedwe kupita ku Babulo.+
-