8 Choncho akuluakulu amenewa anapita kwa Gedaliya ku Mizipa.+ Mayina awo anali Isimaeli+ mwana wa Netaniya, Yohanani+ ndi Yonatani ana a Kareya, Seraya mwana wa Tanumeti, ana a Efai wa ku Netofa, Yezaniya+ mwana wa munthu wa ku Maaka limodzi ndi asilikali awo.