Yeremiya 40:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Gedaliya mwana wa Ahikamu mwana wa Safani analumbira pamaso pa akuluakuluwo ndi asilikali awo kuti: “Musaope kutumikira Akasidi. Zikhalani mʼdzikoli nʼkumatumikira mfumu ya Babulo ndipo zinthu zidzakuyenderani bwino.+
9 Gedaliya mwana wa Ahikamu mwana wa Safani analumbira pamaso pa akuluakuluwo ndi asilikali awo kuti: “Musaope kutumikira Akasidi. Zikhalani mʼdzikoli nʼkumatumikira mfumu ya Babulo ndipo zinthu zidzakuyenderani bwino.+