-
Yeremiya 40:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Choncho Ayuda onse anayamba kubwerera kuchokera kumadera onse kumene anawabalalitsira ndipo anabwera mʼdziko la Yuda kwa Gedaliya ku Mizipa. Iwo anasonkhanitsa vinyo ndi zipatso zamʼchilimwe zochuluka kwambiri.
-