Yeremiya 40:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo anauza Gedaliya kuti: “Kodi sukudziwa kuti Baalisi mfumu ya a Amoni,+ watumiza Isimaeli mwana wa Netaniya kuti adzakuphe?”+ Koma Gedaliya mwana wa Ahikamu sanawakhulupirire.
14 Iwo anauza Gedaliya kuti: “Kodi sukudziwa kuti Baalisi mfumu ya a Amoni,+ watumiza Isimaeli mwana wa Netaniya kuti adzakuphe?”+ Koma Gedaliya mwana wa Ahikamu sanawakhulupirire.