Yeremiya 42:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 imvani mawu a Yehova, inu otsala a Yuda. Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Ngati mwatsimikiza mtima kuti mupite ku Iguputo ndipo mukapitadi nʼkukakhala* kumeneko,
15 imvani mawu a Yehova, inu otsala a Yuda. Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Ngati mwatsimikiza mtima kuti mupite ku Iguputo ndipo mukapitadi nʼkukakhala* kumeneko,