Yeremiya 43:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma Baruki+ mwana wa Neriya ndi amene akukulimbikitsa kuti unene zinthu zofuna kutipweteketsa nʼcholinga choti mutipereke mʼmanja mwa Akasidi kuti atiphe kapena atitenge kupita ku ukapolo ku Babulo.”+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 43:3 Nsanja ya Olonda,8/15/2006, tsa. 19
3 Koma Baruki+ mwana wa Neriya ndi amene akukulimbikitsa kuti unene zinthu zofuna kutipweteketsa nʼcholinga choti mutipereke mʼmanja mwa Akasidi kuti atiphe kapena atitenge kupita ku ukapolo ku Babulo.”+