Yeremiya 43:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mʼmalomwake, Yohanani mwana wa Kareya ndi akuluakulu onse a asilikali anatenga anthu onse amene anatsala ku Yuda amene anabwerera kuchokera ku mitundu yonse ya anthu kumene anathawira kuti adzakhale mʼdziko la Yuda.+
5 Mʼmalomwake, Yohanani mwana wa Kareya ndi akuluakulu onse a asilikali anatenga anthu onse amene anatsala ku Yuda amene anabwerera kuchokera ku mitundu yonse ya anthu kumene anathawira kuti adzakhale mʼdziko la Yuda.+