Yeremiya 44:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ine ndinkakutumizirani mobwerezabwereza* atumiki anga onse amene ndi aneneri. Ndinkawatuma uthenga wakuti: “Chonde, musachite zinthu zonyansazi zimene ndimadana nazo.”+
4 Ine ndinkakutumizirani mobwerezabwereza* atumiki anga onse amene ndi aneneri. Ndinkawatuma uthenga wakuti: “Chonde, musachite zinthu zonyansazi zimene ndimadana nazo.”+